Kukhala Chete Sikuvomeredza

(Aroma 2:4)


“Ngati kuli Mulungu, ndi chifukwa ciani amalolera kuti nyengo zovuta kwambiri kumachitika?” Nthawi zambiri anthu amapereka mafunso otere olamitsa kumiyamba yomwe siyankhapo kanthu. Momwemonso, Pali mafunso ambiri timakhala nao kuti titha kufunsa. “Ndichifukwa ciani Mulungu olungama sasanulira chiwerudzo chake pa nthawi yomweyo, koma m’malo mwake kusungabe anthu ochimwa kotheratu otere?”

1. Kuwawa M’kudikilira
Mulungu amachita ndi anthu monga mwaubwino Wake, mukulekerera mdi muchipiliro. Umu ndi m’mene Mulungu aledza mtima kwa anthu okugwa monga umo munthu achitira ndi mdani wake mofatsa. Amagwirabe chikho chamkwiyo ndi manja ake. Mulungu akhadzikikabe muchikhalidwe Chake cha chiyero ndi kusenza kuwawa konse muchipiliro ngati goli Lake. Ichi chikutsimikidzira kuti Mulungu saima pambali kuonerera, koma ali ochitachita, kumva kuwawa kwakukulu mu choonadi – kulukerera pa ochimwa.

2. Kunyadzitsa Chisomo
Ayuda, anaonongedwa chifukwa chakudzikweza pakuti anapatulidwa pa mtundu wao komanso anapatsidwa Chilamulo, kuchitenga molakwika kulekelera kwa Mulungu n’kumaona ngati iwo ndi opatulidwa ku chiwerudzo. Kodi ife sitichitenga chilengedwe cha Mulungu kukhala chopepuka lero, kuchita machimo mobweredza ndi mwadala chifukwa chilango pa ife sichiperekedwa munthawi yomweyi? Kutenga molakwika kulekerera kwa Mulungu, “kukhala ngati ndichovomeledzedwa,” ndi m’chitidwe opusa omwe unyazitsa komanso kudziyeneredza mopanda kutsimikidzira ndi choonadi cha ubwino Wake. Kukhala ndi machawi kuchita tchimo mtima onyazitsa ndi kumuyankhulira moipa Mulungu.

3. Chiyembekezo Chachigonjetso Kuchokera Mukusalungama
Wapereka ku nyengo ino, chotitsogolera ife mukulapa. Kulapa ndi mdalitso waukulu pa madalitso onse ndipo ndi njira yokhayo yotembenudzira kuwawa kwa Mulungu kukhala chisangalalo. Tiyeni tisachitenge chopepuka, ubwino wa Mulungu omwe utifikitsa ku kulapa, pakubvomereza kwa chiyero Chake ndi kuitanidwa mwa machawi mwachikondi. Tiyeni titengepo gawo mu chiyembekezo  chachigonjetso kuchokera muchosalungama koma monga umo mwa ubwino Wake.

Abusa Sung – Hyun Kim

Januwale 25, 2026 Utumiki wa Tsiku la Ambuye
Inu Amene Mukugwiritsa Ntchito Molasika Kuleza Mtima kwa Mulungu
Aroma 2:4
Abusa Sung-Hyun Kim