Bwalo Lamilandu Lakumwamba Lomwe Chinyengo Sichiloredwa

(Aroma 2:2-3)


Ku dziko lapansi, kuli zosalungama zambiri zomwe odzichitao salandira chilango chowayenera. Omwe akhadzikika mu ntchito zotere kawirikawiri amakhulupilira kuti ntchito zao zoipazo zidzakhululukidwa kopanda wina kudziwa, ndipo nthawi zina akhala mumachitachita obisalira choonadi, Komabe, ngakhale achita monyenga, chiwerudzo cha Mulungu chimalunjika mosogozedwa ndi choonadi.

1. Otsutsa Chilungu Ovala Chigoba
Chidziwitso cha umunthu ndichotsokeretsa kwambiri, moyerekedza ndi kuzindikira ubwino wa Mulungu ndi kudekha mukudikilira. Anthu amatenga chisomo Chake mwachidzolowezi. Nthawi zonse amakhala a changu pa chitsutso cholakwika ndi kukankhidza cholakwacho kwa ena, chonsecho akhadzikika pa choipa ndipo amakhulupilira kuti akunamidza ngakhale Mulungu. Muchiyembekedzo chopanda madziko enieni, amati, “Mulungu ndi wabwino, kutero kuti Iye sadzatitumidza ku Gehena,” Ichi ndi chopsya kukhala muchiwerudzo cholakwika kuchokera ku nzeru yokugwa ya dziko.

2. Chilango Chochulukitsidwa Ku Chinyengo
Chiwerudzo cha Mulungu chimaperekedwa mosogozedwa ndi madziko a choonadi. Mulungu amationa ife mu choonadi pa zonse zomwe timachita, kuphatikidzapo ngakhale zamundima zonse zomwe timayesera kubisa. Ndi muyeso omwe tigwiritsa ntchito kuwerudza ena molakwika ngati umboni udzaima motsutsana nafe, ndipo pakutha pa zonse tidzadzindikira choonadi, omwe awerudza ena kudzitenga iwo olungama mwa iwo okha sadzawerudzidwa chifukwa cha ntchito zao zokha, komanso adzaima pa chiwerudzo chopsya chifukwa cha chinyengo.

3. Kubvomeredza : Njira Yopatuka Pa Chiwerudzo
Ngati omwe analakwira chilamulo choperekedwa kudzera mwa Mose sanapedzeke kukhala osalangidwa, tipulumuka bwanji ngati tidzikanidza ku chipulumutso chamtengo wake kudzera mwa Mwana wa Mulungu? Palibe ngakhale m’modzi yemwe adzapulumuka ku chiwerudzo cha Mulungu. Njira yokhayo yopedzera moyo ndi kuthawira mu ulemerero mwa Yesu Kristu, Iye anamwera chikho cha chiwerudzo m’malo mwathu, kulapa kuchokera pansi pa mtima – ndi kudzionetsera tokha mu kukhulupilika konse kwa Mulungu ndi kuyeretsedwa ndi Mzimu wa Mulungu – chiyembekedzo chathu chokhacho chotilanditsa ku mpando wa chiwerudzo kutifikitsa ku moyo wosatha.

Abusa Sung – Hyun Kim

Januwale 11, 2026 Utumiki wa Tsiku la Ambuye
Inu Omwe Muweruza Ena
Aroma 2:1
Abusa Sung-Hyun Kim