OWERUDZA MOPANDA KUZENGEREDZA

(Aroma 3:4-6)


Munakhalapo olakwira chilungamo koma kupedzeka kuti mwakonderedwa ? Mosasamalira kuti mukudziyankhulira mu nzeru yozama motani – munthu winayo amayeserabe kudzidzembaisa mu mau ako kufikira ataonetsera kuti uli munthu woipa kwambiri. Izi zili chimodzimodzi ndi nyengo za Paulo. Amalalikira za Uthenga Wabwino wa Yesu Kristu – Uthenga umagogomedzera za chisomo moyerekedzera ndi ntchito – koma Ayuda ena anaima motsutsana ndi iye, kuyetsera kudzidzembaisa mukuyankhula kwawo mosalekedza.

1. Malonjedzo Sadzaimitsidwa
Ayuda anayankhula motere, “Mulungu analonjedza kudalitsa ife – kotero  ndi chifukwa ciani mumaphunzitsa kuti naonso Ayuda awerudzidwa pa machimo awo? Kodi simukuthetsa malonjedzo Ache?” Yankho la Paulo linali lolunjika, “Ayi ndithu” Pachoonadi choti tchimo limabweretsa chiwerudzo, izi zili muyeso umodzi ngakhale pa Ayuda, – komanso chifukwa choti Mulungu ndi okhulupirika osunga pangano – chilungamo chiwiri ichi sichidzaima motsutsana, kotero zonse zili zoona munthawi imodzi yomweyi.

2. Chilungamo Sichidzengeredza
Ayuda ananenanso modzembaitsa, “Ngati chisalungamo chathu chionetsera chilungamo cha Mulungu, Kodi sikukhala kupanda chilungamo pa Iye pa kutsanulira mkwiyo wake pa ife?” Paulo analibe china chonenapo koma anati, “Ayi ndithu sichoncho” Chilungamo cha Mulungu sichili chinthu chomwe chimaonekera bwino pochiyerekedza ndi tchimo la anthu. Amawerudza osalungama ndi chilungamo choonadi – nthawi zonse, mosakondera, mkwiyo wake suima ngati kuipa kwa Iye, koma chili choima kutsimikidzira kulungama Kwake.

3. Kudzinenerera Nkosaloledwa
Ayuda analimbana naye komalidza, “Mukutanthaudza kunena kuti  -“Tidzichitabe choipacho ndipo chabwinocho chitsatira?” Paulo anayankha mopanda kudzembaitsa nati, “Kutsutsidwa kwanu ndi kwa chilungamo, kodi simunalingalirepo mwa inu nokha, ndi kuti, “cholinga changa chinali chabwino koma kuti ndadzichita izo mu njira yolakwika. Mulungu adzadzilekerera. Kotero kuti sadzalola kuti ndimilire pa chiwerudzo?” Umu ndi momwe onse omwe amatsutsana ndi Paulo anaimira. Chilungamo chomwe tiyenera kuimapo ndi ichi, tiyenera kubvomeredza chilungamo Chake ndi kudzikhulupilira mwa ife tokha mu chisomo Chake chonse.

Abusa Sung – Hyun Kim

Epulo 19, 2026 Utumiki wa Tsiku la Ambuye
Chiweruzo Cholungama cha Mulungu Chosasinthika
Aroma 3:4-6
Abusa Sung-Hyun Kim